Afilipi 3:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

kuti ndimzindikire iye, ndi mphamvu ya kuuka kwace, ndi ciyanjano ca zowawa zace, pofanizidwa ndi imfa yace;

Afilipi 3

Afilipi 3:9-15