Afilipi 3:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Cotsalira, abale anga, kondwerani mwa Ambuye. Kulembera zomwezo kwa inu, sikundibvuta ine, koma kwa inu kuli kukhazikitsa.

2. Penyererani agaru, penyererani ocita zoipa, penyererani coduladula;

3. pakuti ife ndife mdulidwe, akutumikira popembedza ndi Mzimu wa Mulungu, nadzitamandira mwa Yesu Kristu, osakhulupirira m'thupi;

Afilipi 3