Afilipi 2:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma ndinayesa nkufunika kutuma kwa inu Epafrodito mbaleyo, ndiye wanchito mnzanga ndi msilikari mnzanga, ndiye mtumwi wanu, ndi wonditumikira pa cosowa canga;

Afilipi 2

Afilipi 2:17-27