Afilipi 2:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma muzindikira matsimikizidwe ace, kuti, monga mwana acitira atate wace, anatumikira pamodzi ndi ine Uthenga Wabwino.

Afilipi 2

Afilipi 2:14-27