Afilipi 2:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

kuti mukakhale osalakwa ndi oona, ana a Mulungu opanda cirema pakati pa mbadwo wokhotakhota ndi wopotoka, mwa iwo amene muonekera monga mauniko m'dziko lapansi,

Afilipi 2

Afilipi 2:11-20