Aefeso 6:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Ananu, mverani akukubalani mwa Ambuye, pakuti ici ncabwino. Lemekeza atate wako ndi amako (ndilo lamulo loyamba