Aefeso 5:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Cifukwa cace khalani akutsanza a Mulungu, monga ana okondedwa;

2. ndipo yendani m'cikondi monganso Kristu anakukondani inu, nadzipereka yekha m'malo mwathu, copereka ndi nsembe kwa Mulungu, ikhale pfungo lonunkhira bwino.

Aefeso 5