Aefeso 4:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mwa ici, mutataya zonama, 3 lankhulani zoona yense ndi mnzace; 4 pakuti tiri ziwalo wina ndi mnzace.

Aefeso 4

Aefeso 4:18-31