Aefeso 4:20-22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

20. Koma inusimunaphunzira Kristu cotero,

21. ngatitu mudamva iye, ndipo munaphunzitsidwa mwa iye, monga coonadi ciri mwa Yesu;

22. kuti mubvule, kunena za makhalidwe anu oyamba, munthu wakale, wobvunda potsata zilakolako za cinyengo;

Aefeso 4