Aefeso 4:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kuti tisakhalenso makanda, ogwedezekagwedezeka, natengeka-tengeka ndi mphepo yonse ya ciphunzitso, ndi tsenga la anthu, ndi kucenjerera kukatsata cinyengo ca kusoceretsa;

Aefeso 4

Aefeso 4:4-24