Aefeso 3:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Cifukwa ca ici ine Paulo, ndine wandende wa Kristu Yesu cifukwa ca inu amitundu,

2. ngatitu munamva za udindo wa cisomo ca Mulungucimene anandipatsa ine ca kwa inu;

Aefeso 3