2 Yohane 1:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yense wakupitirira, wosakhala m'ciphunzitso ca Kristu, alibe Mulungu; iye wakukhala m'ciphunzitso, iyeyo ali nao Arate ndi Mwana.

2 Yohane 1

2 Yohane 1:1-11