2 Timoteo 3:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo monga momwe Yane ndi Yambre anatsutsana naye Mose, kotero iwonso atsutsana naco coonadi; ndiwo anthu obvunditsitsa mtima, osatsimikizidwa pacikhulupiriro.

2 Timoteo 3

2 Timoteo 3:1-17