2 Timoteo 2:25-26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

25. 1 wolangiza iwo akutsutsana mofatsa; 2 ngati kapena Mulungu awapatse iwo citembenuziro, kukazindikira coonadi,

26. ndipo 3 akadzipulumutse ku msampha wa mdierekezi, m'mene anagwidwa naye, ku cifuniro cace.

2 Timoteo 2