2 Timoteo 2:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Uwakumbutse izi, ndi kuwacitira umboni pamaso pa Ambuye, kuti asacite makani ndi mau osapindulitsa kanthu, koma ogwetsa iwo akumva.

2 Timoteo 2

2 Timoteo 2:11-19