2 Timoteo 2:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mwa ici ndipirira zonse, cifukwa ca osankhika, kuti iwonso akapeze cipulumutsoeo ca mwa Kristu Yesu, pamodzi ndi ulemerero wosatha.

2 Timoteo 2

2 Timoteo 2:8-11