2 Samueli 9:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mefiboseti mwana wa Jonatani, mwana wa Sauli, anafika kwa Davide, nagwa nkhope yace pansi, namlambira. Ndipo Davide anati, Mefiboseti! Nayankha iye, Ndine mnyamata wanu.

2 Samueli 9

2 Samueli 9:1-9