2 Samueli 9:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mefiboseti anali ndi mwana wamwamuna wamng'ono, dzina lace ndiye Mika. Ndipo onse akukhala m'nyumba ya Ziba anali anyamata a Mefiboseti.

2 Samueli 9

2 Samueli 9:11-13