2 Samueli 8:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Davide anakanthanso Hadadezeri, mwana wa Rehobu, mfumu ya ku Zoba, pomuka iye kukadzitengeranso ufumu wace ku cimtsinje ca Firate.

2 Samueli 8

2 Samueli 8:1-5