2 Samueli 7:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinali nawe kuli konse unamukako, ndi kuononga adani ako onse pamaso pako; ndipo ndidzamveketsa dzina lako, monga dzina la akuru ali pa dziko lapansi,

2 Samueli 7

2 Samueli 7:8-11