2 Samueli 7:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mwadzikhazikira anthu anu Aisrayeli, akhale anthu anu nthawi zonse, ndipo Inu Yehova munakhala Mulungu wao.

2 Samueli 7

2 Samueli 7:19-28