2 Samueli 7:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo icinso cinali pamaso panu cinthu cacing'ono, Yehova Mulungu; koma munanenanso za banja la mnyamata wanu kufikira nthawi yaikuru irinkudza; ndipo mwatero monga mwa macitidwe a anthu, Yehova Mulungu!

2 Samueli 7

2 Samueli 7:15-29