2 Samueli 7:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo nyumba yako ndi ufumu wako zidzakhazikikadi ku nthawi zonse pamaso pako; mpando wacifumu wako udzakhazikika ku nthawi zonse.

2 Samueli 7

2 Samueli 7:14-25