2 Samueli 7:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamene masiku ako akadzakwaniridwa, ndipo iwe udzagona ndi makolo ako, Ine ndidzaukitsa mbeu yako pambuyo pako, imene idzaturuka m'matumbo mwako, ndipo ndidzakhazikitsa ufumu wace.

2 Samueli 7

2 Samueli 7:9-15