2 Samueli 6:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Momwemo Davide sanafuna kudzitengera likasa la Yehova lidze ku mudzi wa Davide; koma Davide analipambutsira ku nyumba ya Obedi-Edomu Mgiti.

2 Samueli 6

2 Samueli 6:2-13