2 Samueli 5:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kudzali, pakumva iwe kuwayula ku nsonga za mkandankhuku, pomwepo fulumiratu, pakuti pamenepo Yehova waturuka pamaso pako kukakantha khamu la Afilisti.

2 Samueli 5

2 Samueli 5:16-25