2 Samueli 4:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide analamulira anyamata ace, iwo nawapha, nawapacika m'mbali mwa thamanda ku Hebroni atawadula manja ndi mapazi ao. Koma mutu wa Isiboseti anautenga nauika m'manda a Abineri ku Hebroni.

2 Samueli 4

2 Samueli 4:5-12