2 Samueli 3:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Sauli adali ndi mkazi wamng'ono, dzina lace ndiye Rizipa, mwana wa Aya. Ndipo Isiboseti anati kwa Abineri, Unalowana bwanji ndi mkazi wamng'ono wa atate wanga?

2 Samueli 3

2 Samueli 3:6-12