2 Samueli 3:37 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Momwemo anthu onse ndi Aisrayeli onse anazindikira tsiku lija kuti sikunafumira kwa mfumu kupha Abineri mwana wa Neri.

2 Samueli 3

2 Samueli 3:32-38