2 Samueli 3:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide anati kwa Yoabu ndi kwa anthu onse okhala naye, Ng'ambani zobvala zanu, ndi kudzimangira ziguduli m'cuuno, nimulire Abineri. Ndipo mfumu Davide anatsata cithatha.

2 Samueli 3

2 Samueli 3:21-39