2 Samueli 3:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pofikanso Abineri ku Hebroni, Yoabu anampambutsa kupita nave pakati pa cipata kulankhula naye poduka mphepo; namgwaza pomwepo m'mimba, nafa, cifukwa ca mwazi wa Asaheli mbale wace.

2 Samueli 3

2 Samueli 3:18-28