2 Samueli 3:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mumdziwa Abineri mwana wa Neri kuti anadza kuti akunyengeni, ndi kuti adziwe kuturuka kwanu ndi kulowa kwanu, ndi kuti adziwe zonse mulikucita inu.

2 Samueli 3

2 Samueli 3:24-35