2 Samueli 3:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsono pofika Yoabu ndi khamu lonse anali nalo, ena anamfotokozera Yoabu nati, Abineri mwana wa Neri anabwera kwa mfumu, amene analawirana naye, namuka iye mumtendereo

2 Samueli 3

2 Samueli 3:15-33