2 Samueli 3:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide anatumiza mithenga kwa Isiboseti mwana wa Sauli, nati, Undipatse mkazi wanga Mikala amene ndinadzitomera ndi nsonga za makungu za Afilisti zana limodzi.

2 Samueli 3

2 Samueli 3:11-16