2 Samueli 24:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma mau a mfumu anapambana Yoabu ndi atsogoleri a khamulo. Ndipo Yoabu ndi atsogoleri a khamulo anaturuka pamaso pa mfumu kuti akawerenge anthu a Israyeli.

2 Samueli 24

2 Samueli 24:2-12