2 Samueli 24:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide anamangirapo Yehova guwa la nsembe, napereka nsembe zopsereza, ndi nsembe zoyamika. Momwemo Yehova anapembedzeka cifukwa ca dziko, ndi mliri wa pa Israyeli unalekeka.

2 Samueli 24

2 Samueli 24:19-25