2 Samueli 24:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Arauna nati, Mbuye wanga mfumu, mwadzeranji kwa mnyamata wanu? Ndipo Davide anati, Kugula dwale lako gi, kuti ndimangirepo Yehova guwa lansembe, kuti mliriwo ulekeke kwa anthu.

2 Samueli 24

2 Samueli 24:15-25