2 Samueli 24:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide analankhula ndi Yehova pamene anaona mthenga wakudwalitsa anthu, nati, Onani ndacimwa ine, ndinacita mwamphulupulu; koma nkhosa izi zinacitanji? dzanja lanu likhale pa ine ndi pa nyumba ya atate wanga.

2 Samueli 24

2 Samueli 24:13-19