2 Samueli 23:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Benaya, mwana wa Yehoyada, mwana wa ngwazi wa ku Kabzeli amene anacita zamphamvu; iye anapha anthu awiri a Moabu akunga mikango, natsikanso iye napha mkango m'mbuna nyengo ya cipale cofewa;

2 Samueli 23

2 Samueli 23:12-25