2 Samueli 23:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

iye ananyamuka, nakantha Afilisti kufikira dzanja lace linalema, ndi dzanja lace lomamatika kulupanga; ndipo Yehova anacititsa cipulumutso cacikuru tsiku lija, ndipo anthu anabwera m'mbuyo mwace kukafunkha kokha.

2 Samueli 23

2 Samueli 23:1-12