2 Samueli 22:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kunena za Mulungu, njira yace iri yangwiro;Mau a Yehova anayesedwa; iye ndiye cikopa kwa onse akukhulupirira iye.

2 Samueli 22

2 Samueli 22:29-38