2 Samueli 21:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma mfumu inaleka Mefiboseti mwana wa Jonatani, mwana wa Sauli, cifukwa ca lumbiro la kwa Yehova linali pakati pa Davide ndi Jonatani mwana wa Sauli.

2 Samueli 21

2 Samueli 21:1-9