2 Samueli 21:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo panalinso nkhondo ndi Afilisti ku Gobu; ndipo Elhanani mwana wa Jare-oregimu wa ku Betelehemu anapha Goliate Mgiti, amene mtengo wa mkondo wace unanga mtanda wa woombera nsaru.

2 Samueli 21

2 Samueli 21:18-22