2 Samueli 21:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Isibenobi, ndiye wa ana a Rafa, amene kulemera kwa mkondo wace kunali masekeli mazana atatu a mkuwa, iyeyo anabvala lupanga latsopano, nati aphe Davide.

2 Samueli 21

2 Samueli 21:15-22