2 Samueli 20:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yoabu ananena ndi Amasa, Uli bwino mbale wanga? Ndipo Yoabu anagwira ndebvu za Amasa ndi dzanja lace lamanja kuti ampsompsone.

2 Samueli 20

2 Samueli 20:6-13