2 Samueli 20:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Comweco anthu onse a Israyeli analeka kutsata Davide, natsata Seba mwana wa Bikri; koma anthu a Yuda anaphatikizana ndi mfumu yao, kuyambira ku Yordano kufikira ku Yerusalemu.

2 Samueli 20

2 Samueli 20:1-6