2 Samueli 20:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mnyamata wina wa Yoabu anaima pali iye, nati, Wobvomereza Yoabu, ndi iye amene ali wace wa Davide, atsate Yoabu.

2 Samueli 20

2 Samueli 20:9-19