2 Samueli 2:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo tsopano Yehova acitire inu cokoma ndi coonadi; inenso ndidzakubwezerani cokoma ici, popeza munacita cinthuci.

2 Samueli 2

2 Samueli 2:1-12