2 Samueli 2:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi Yoabu mwana wa Zeruya, ndi anyamata a Davide anaturuka nakomana nao pa thamanda la Gibeoni; nakhala pansi, ena tsidya lino, ndi ena tsidya lija la thamandalo.

2 Samueli 2

2 Samueli 2:5-20