2 Samueli 2:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide anali mfumu ya nyumba ya Yuda ku Hebroni zaka zisanu ndi ziwiri kudza miyezi isanu ndi umodzi.

2 Samueli 2

2 Samueli 2:10-15